Bible News Prophecy Magazine in Chichewa Apr-Jun 2018

M’magazini Ino:
3 Kuchokera Mkonzi: KODI MPINGO WOONA WA MULUNGU NDI WOYENERA KUKHALA NDI LIKULU LAKE KU YERUSALEMU? Anthu ena akumatero. Kodi nanga baibulo likutiphunzitsa kuti chiyani?

13 TIYENI TIWERENGE PHUNZIRO 13 LA BAIBULO: Kodi cholowa cha Akhristu chiani? Kodi akhristu adzalandira cholowa chawo pa dziko lapansi kapena kumwamba?

28 Kodi chipangano chakale chikutiphunzitsa chiani za Ufumu wa Mulungu? Kodi ana Aisraeli amadziwa za Ufumu wa Mulungu kuchokera mu malemba a chihebri?

31 SITIDZATHAWA CHITSAUTSO CHA CHIKULUCHO! Mtumiki wakale Leroy Neff analemba zokhuzana ndi nkhaniyi zaka zapitazi. Matsiku alerowa zili kutsonyeza kuti tili mu nthawi ya zitsautso zazikulu.

CHIKUTIRO CHA KUNJA: intaneti ndi wayilesi zikusonyeza mene mungapedzere ma mauthenga kuchokera mu Mpingo woona wa Mulungu.

Pano pali kulumikizana kwa magazini: Nkhani Za Ulosi M BAIBULO April – June 2018

Posted in CCOG Africa News, Magazines